Phi!! Yagwanso Malawi Kwacha
Nyimbo yake mwina nkukhala ya “timalizeni, tatsala pati?” kapena mwina ija ya pa mauthenga a chisoni ya “Atimwe”. Banki yaikulu ya mu dziko muno yaswa nkhonya ina yowawa: Malawi Kwacha yagwanso.
Welengani nkhaniyi apa: https://malawi24.com/2024/03/20/phi-yagwanso-malawi-kwacha/
#national business news
Add comment
You will be commenting as Guest.
Your email address will not be published.
Leave a Reply