Malipoti akuti Nankhumwa akubwela ndi chake chipani: PDP
Nonse othodwa ndi zipani zonse zilipo pano, ena chabe ongokhala okondwa ndi bambo Kondwani Nankhumwa ndipo mumafunitsitsa atalamula dziko lino, musataye mtima kwenikweni. Chipani chatsopano chikubwela. Okamba akuti ndi cha a Kondwani Nankhumwa. Dzina lake ndi PDP, People’s Development Party.
Werengani nkhani yonse: https://malawi24.com/2024/03/21/malipoti-akuti-nankhumwa-akubwela-ndi-chake-chipani-pdp/
#Politics News
Add comment
You will be commenting as Guest.
Your email address will not be published.
Leave a Reply