Wayamba kukwaniritsa malonjezo Haiya: chithumba cha ligi chakwera
…owina tsopano azitenga MK100 miliyoni
…yonse pamodzi yafika pa MK500 miliyoni
Koma apambane ligi chaka chino adya bwino. Yamasula ma bureki TNM, chithumba cha ligi angokhuthula. Malonjezo a Fleetwood Haiya mmbalimo akukwanitsidwa.
Welengani nkhaniyi apa: https://malawi24.com/2024/04/24/wayamba-kukwaniritsa-malonjezo-haiya-chithumba-cha-ligi-chakwera/
#Sports news
Add comment
You will be commenting as Guest.
Your email address will not be published.
Leave a Reply