Awiri anjata pofuna kulowetsa chamba ku ndende
Mnyamata wina yemwe amayankha mlandu kale, wamangidwaso kachiwiri pamodzi ndi mzake wina yemwe amafuna kukamupatsira chamba chomwe anachibisa munkhwayira tsiku lakumva mlandu.
Werengani nkhani yonse apa: https://malawi24.com/2024/04/18/awiri-anjata-pofuna-kulowetsa-chamba-ku-ndende/
Add comment
You will be commenting as Guest.
Your email address will not be published.
Leave a Reply