Kusowa kwa Shuga kwafika povuta mu mzinda wa Zomba
…Ena adandaula kuti bizinesi yawo yophika kachasu yaima
Anthu ochuluka adasonkhana mu shopu ya Chipiku Plus mu mzinda wa Zomba kukanganirana kugula shuga ndipo anthu amakhala maola atatu ali pa mzere asadagule.
Werengani nkhani yonse apa: https://malawi24.com/2024/03/21/kusowa-kwa-shuga-kwafika-povuta-mu-nzinda-wa-zomba/
#national news
Add comment
You will be commenting as Guest.
Your email address will not be published.
Leave a Reply