Upepese, apo bii ndichita china chake – Zani Challe waopseza Tuno
…Tuno akuloza chala mowa omwe anamwa
Kuli chinkulirano pakati pa oyimba Zani Challe yemwe lero watulutsa chikalata chomuuza oyimba Tuno kuti amupepese apo bii apanga chinthu china chomwe sananene ati kamba komunena kuti iye amagulitsa thupi komaso amachita malonda a mankhwala ozunguza ubongo.
Werengani nkhani yonse apa: https://malawi24.com/2024/03/13/upepese-apo-bii-ndichita-china-chake-zani-challe-waopseza-tuno/
#entertainment news
Add comment
You will be commenting as Guest.
Your email address will not be published.
Leave a Reply